33 Eleazarenso mwana wa Aroni anafa; ndipo anamuika pa phiri la Pinehasi mwana wace, limene adampatsa ku mapiri a Efraimu.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 24
Onani Yoswa 24:33 nkhani