Yoswa 3:1 BL92

1 Ndipo Yoswa analawirira mamawa, kucoka ku Sitimu, nafika ku Yordano, iye ndi ana onse a Israyeli; nagona komweko, asanaoloke.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 3

Onani Yoswa 3:1 nkhani