6 Ndipo Yoswa anati kwa ansembe, Senzani likasa la cipangano, nimuoloke pamaso pa anthu. Nasenza iwo likasa la cipangano, natsogolera anthu.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 3
Onani Yoswa 3:6 nkhani