4 Koma cifukwa cakuti Yoswa anawadula ndi ici: anthu onse oturuka m'Aigupto, anthu amuna, ndiwo amuna onse ankhondo, adafa m'cipululu panjira, ataturuka m'Aigupto.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 5
Onani Yoswa 5:4 nkhani