25 Ndipo Yoswa anati, Watisautsiranji? Yehova adzakusautsa lero lino. Ndipo, Aisrayeli onse anamponya miyala, nawatentha ndi moto, nawaponya miyala.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 7
Onani Yoswa 7:25 nkhani