6 Ndipo Yoswa anang'amba zobvala zace, nagwa nkhope yace pansi, ku likasa la Yehova, mpaka madzulo, iye ndi akulu akulu a Israyeli, nathira pfumbi pamitu pao.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 7
Onani Yoswa 7:6 nkhani