Yoswa 8:13 BL92

13 Momwemo anaika anthu, khamu lonse lokhala kumpoto kwa mudzi, ndi olalira ao kumadzulo kwa mudzi, ndipo usiku uja Yoswa analowa pakati pa cigwa,

Werengani mutu wathunthu Yoswa 8

Onani Yoswa 8:13 nkhani