Yoswa 9:27 BL92

27 Ndipo tsiku lija Yoswa anawasandutsa akutema nkhuni, ndi otungira madzi msonkhanowo, ndi guwa la nsembe la Yehova, mpaka lero lino, pamalopo akadzasankha.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 9

Onani Yoswa 9:27 nkhani