6 Ndipo zinamuka kwa Yoswa kumisasa ku Giligala, niziti kwa iye ndi kwa amuna a Israyeli, Tacokera dziko lakutali, cifukwa cace mupangane nafe.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 9
Onani Yoswa 9:6 nkhani