32 Ndipo mfumu Davide anati, Kandiitanireni Zadoki wansembeyo, ndi Natani mneneriyo, ndi Benaya mwana wa Yehoyada. Iwo nalowa pamaso pa mfumu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1
Onani 1 Mafumu 1:32 nkhani