33 Ndipo mfumu inati kwa iwo, Tengani akapolo a mfumu yanu, nimukweze Solomo mwana wanga pa nyuru yanga yanga, nimutsikire naye ku Gihoni.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1
Onani 1 Mafumu 1:33 nkhani