1 Mafumu 1:35 BL92

35 Pamenepo mumtsate iye, iye nadzadza nadzakhala pa mpando wanga wacifumu, popeza adzakhala iyeyu mfumu m'malo mwanga; ndipo ndamuika iye akhale mtsogoleri wa lsrayeli ndi Yuda.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:35 nkhani