1 Mafumu 1:8 BL92

8 Koma Zadoki wansembe, ndi Benaya mwana wace wa Yehoyada, ndi Natani mneneri, ndi Simeyi, ndi Reyi, ndi anthu amphamvu aja adali ndi Davide, sanali ndi Adoniya.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:8 nkhani