1 Mafumu 1:9 BL92

9 Ndipo Adoniya anapha nkhosa ndi ng'ombe ndi nyama zonona pamwala pa Zoheleti, uli pafupi ndi citsime ca Rogeli, naitana abale ace onse ana a mfumu, ndi anthu onse a Yuda anayamata a mfumu;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 1

Onani 1 Mafumu 1:9 nkhani