1 Mafumu 10:1 BL92

1 Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Seba mbiri ya Solomo yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi yododometsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 10

Onani 1 Mafumu 10:1 nkhani