13 komatu sindidzacotsa ufumu wonsewo; pfuko limodzi ndidzapatsa mwana wako, cifukwa ca Davide mtumiki wanga, ndi cifukwa ca Yerusalemu amene ndinamsankha.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11
Onani 1 Mafumu 11:13 nkhani