1 Mafumu 11:14 BL92

14 Ndipo Yehova anamuutsira Solomo mdani, ndiye Hadadi M-edomu; iyeyo anali wa mbumba ya mfumu ya ku Edomu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11

Onani 1 Mafumu 11:14 nkhani