19 Ndipo Farao anamkomera mtima ndithu Hadadiyo, nampatsa mkazi ndiye mbale wa mkazi wace, mbale wace wa Takipenesi mkazi wamkulu wa mfumu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 11
Onani 1 Mafumu 11:19 nkhani