1 Mafumu 12:11 BL92

11 Ndipo tsopano, popeza atate wanga anakusenzani gori lolemera, ine ndidzaonjezerapo pa gori lanu, atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:11 nkhani