1 Mafumu 12:28 BL92

28 Potero mfumu inakhala upo, napanga ana a ng'ombe awiri agolidi, nati kwa iwo, Kukulemetsani kukwera ku Yerusalemu; tapenyani Aisrayeli inu milungu yanu imene inakuturutsani m'dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:28 nkhani