1 Mafumu 12:33 BL92

33 Ndipo anapereka nsembe pa guwa la nsembe analimanga m'Beteli, tsiku lakhumi ndi cisanu la mwezi wacisanu ndi citatu, m'mwezi umene anaulingirira m'mtima mwa iye yekha, nawaikira ana a Israyeli madyerero, napereka nsembe pa guwa la nsembe, nafukiza zonunkhira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 12

Onani 1 Mafumu 12:33 nkhani