1 Mafumu 13:1 BL92

1 Ndipo onani, munthu wa Mulungu anacokera ku Yuda mwa mau a Yehova nadza ku Beteli; ndipo Yerobiamu anali kuimirira m'mbali mwa guwa la nsembe kufukiza zonunkhira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:1 nkhani