1 Mafumu 13:12 BL92

12 Ndipo atate wao anati kwa iwo, Wapitira njira yiti? popeza ana ace adaona njira analowera munthu wa Mulungu anacokera ku Yudayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:12 nkhani