1 Mafumu 13:17 BL92

17 pakuti mau a Yehova anadza kwa ine, nati Usakadye mkate, kapena kumwa madzi kumeneko, kapena kubwerera njira yomweyo unadzerayo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:17 nkhani