24 Ndipo atacoka iye, mkango unakomana naye panjira, numupha, ndipo mtembo wace unagwera m'njiramo, buru naima pafupi, mkangonso unaima pafupi ndi mtembo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:24 nkhani