25 Ndipo onani, anthu anapitapo naona mtembo wogwera m'njiramo, ndi mkango uli ciimire pafupi ndi mtembo, nadzanena m'mudzi m'mene munakhala mneneri wokalamba uja.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13
Onani 1 Mafumu 13:25 nkhani