1 Mafumu 13:6 BL92

6 Ndipo mfumu inayankha niti kwa munthu wa Mulungu, Undipembedzere Yehova Mulungu wako, nundipempherere, kuti dzanja langa libwerenso kwa ine. Ndipo munthuyo wa Mulungu anapembedza Yehova, ndipo dzanja la mfumu linabwezedwa kwa iye momwemo mwa kale.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:6 nkhani