1 Mafumu 13:5 BL92

5 Ndiponso guwalo linang'ambika, ndi phulusa la pa guwalo linatayika, monga mwa cizindikilo cimene munthu wa Mulungu anapatsa mwa mau a Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 13

Onani 1 Mafumu 13:5 nkhani