19 Ndipo macitidwe ena a Yerobiamu m'mene umo anacitira nkhondo, ndi m'mene umo anacitira ufumu, taona, analembedwa m'buku la macitidwe a mafumu a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14
Onani 1 Mafumu 14:19 nkhani