1 Mafumu 14:20 BL92

20 Ndipo masiku akukhala Yerobiamu mfumu anali zaka makumi awiri mphambu ziwiri, nagona iye kwa makolo ace, nalowa ufumu m'malo mwace Nadabu mwana wace.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:20 nkhani