1 Mafumu 14:2 BL92

2 Ndipo Yerobiamu ananena ndi mkazi wace, Unyamuke, nudzizimbaitse, ungadziwike kuti ndiwe mkazi wa Yerobiamu, nupite ku Silo; taona, kumeneko kuli Ahiya mneneri uja anandiuza ine ndidzakhala mfumu ya anthu awa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:2 nkhani