3 Nupite nayo mikate khumi, ndi timitanda, ndi cigulu ca uci, numuke kwa iye; adzakuuza m'mene umo akhalire mwanayo.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14
Onani 1 Mafumu 14:3 nkhani