4 Natero mkazi wa Yerobiamu, nanyamuka namka ku Silo, nalowa m'nyumba ya Ahiya. Koma Ahiya sanatha kupenya, popeza maso ace anali tong'o, cifukwa ca ukalamba wace.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14
Onani 1 Mafumu 14:4 nkhani