1 Mafumu 14:5 BL92

5 Ndipo Yehova ananena ndi Ahiya, Taona, mkazi wa Yerobiamu akudza kukufunsa za mwana wace, popeza adwala; udzanena naye mwakuti mwakuti; popeza kudzakhala pakulowa iye adzadzizimbaitsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:5 nkhani