1 Mafumu 14:23 BL92

23 Pakuti anadzimangiranso misanje, ndi zoimiritsa, ndi zifanizo, pa citunda conse cacitali, ndi patsinde pa mtengo wogudira uli wonse;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:23 nkhani