24 panalinso anyamata ocitirana dama m'dzikomo; iwo amacita monga mwa zonyansitsa za amitundu, amene Yehova anapitikitsa pamaso pa ana a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14
Onani 1 Mafumu 14:24 nkhani