1 Mafumu 14:25 BL92

25 Ndipo kunacitika, Rebabiamu atakhala mfumu zaka zisanu, Sisaki mfumu ya Aigupto anakwera ndi nkhondo ku Yerusalemu,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 14

Onani 1 Mafumu 14:25 nkhani