1 Mafumu 15:10 BL92

10 Nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai mphambu cimodzi, ndipo dzina la amace linali Maaka mwana wa Abisalomu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 15

Onani 1 Mafumu 15:10 nkhani