1 Mafumu 17:13 BL92

13 Ndipo Eliya anati kwa iye, Usacita mantha, kacite monga umo wanenamo, koma thanga wandiocerako kamkate, nubwere nako kwa ine; ndipo utatero udziphikire wekha ndi mwana wako.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:13 nkhani