14 Popeza atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Mbiya ya ufa siidzatha, ndipo nsupa ya mafuta siidzacepa, kufikira tsiku lakugwetsa mvula Yehova pa dziko lapansi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17
Onani 1 Mafumu 17:14 nkhani