1 Mafumu 17:19 BL92

19 Ndipo ananena naye, Ndipatse mwana wako. Namtenga m'mfukato mwace napita naye ku cipinda cosanja cogonamo iyeyo; namgoneka pa kama wa iye mwini.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:19 nkhani