1 Mafumu 17:20 BL92

20 Napfuulira kwa Yehova, nati, Yehova Mulungu wanga, kodi mwamgwetsera coipa mkazi wamasiye amene ndikhala naye, kumphera mwanace?

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 17

Onani 1 Mafumu 17:20 nkhani