1 Mafumu 18:21 BL92

21 Ndipo Eliya anayandikira kwa anthu onse, nati, Mukayika-kayika kufikira liti? ngati Yehova ndiye Mulungu, mtsateni iye; ngati Baala, mumtsate iyeyo. Ndipo anthu nnena kumyankha mau amodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:21 nkhani