1 Mafumu 18:22 BL92

22 Ndipo Eliya ananena ndi anthuwo, Ine ndatsala ndekha mneneri wa Yehova, koma aneneri a Baala ndiwo anthu mazana anai mphambu makumi asanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:22 nkhani