1 Mafumu 18:46 BL92

46 Ndipo dzanja la Yehova tinakhala pa Eliya; namanga iye za m'cuuno mwace, nathamanga m'tsogolo mwa Ahabu ku cipata ca Yezreeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:46 nkhani