1 Mafumu 19:1 BL92

1 Ndipo Ahabu anauza Yezebeli zonse anazicita Eliya, ndi m'mene anawaphera ndi lupanga aneneri onsewo,

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:1 nkhani