1 Mafumu 18:6 BL92

6 Tsono iwo awiri anagawana dziko kukaliyendera; Ahabu anadzera njira yace yekha, ndi Obadiya njira yina yekha.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18

Onani 1 Mafumu 18:6 nkhani