7 Ndipo Obadiya ali m'njira, taona, Eliya anakomana naye; iye namdziwa, namgwadira, nati, Ndinu kodi mbuye wanga Eliya?
Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 18
Onani 1 Mafumu 18:7 nkhani