1 Mafumu 19:21 BL92

21 Ndipo anabwerera panali iye uja, natengako ng'ombe ziwiri, nazipha, naphikira nyama yace ndi zipangizo za zocitira nazo ng'ombe, napatsa anthu adye. Atatero, ananyamuka, natsata Eliya, namtumikira.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 19

Onani 1 Mafumu 19:21 nkhani