1 Mafumu 20:1 BL92

1 Ndipo Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lace lonse la nkhondo; ndi mafumu makumi atatu mphambu awiri anali naye, pamodzi ndi akavalo ndi magareta; nakamangira Samaria misasa, naponyana nao nkhondo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 20

Onani 1 Mafumu 20:1 nkhani